Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 13:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 (Dera loyambira kukamtsinje kotuluka mu Nailo kum’mawa kwa Iguputo, kukafika kumpoto kumalire ndi Ekironi,+ ankalitcha dziko la Akanani.)+ Madera a Afilisitiwa akulamulidwa ndi olamulira ogwirizana asanu.+ Maderawo ndi Gaza,+ Asidodi,+ Asikeloni,+ Gati+ ndi Ekironi,+ komanso Aavi+ akukhala komweko.

  • 1 Samueli 5:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Choncho anatumiza likasa la Mulungu woona ku Ekironi.+ Ndiyeno likasa la Mulungu woona litangofika ku Ekironi, anthu a ku Ekironi anayamba kulira, kuti: “Atibweretsera likasa la Mulungu wa Isiraeli kuti atiphe ife tonse!”+

  • 2 Mafumu 1:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Kenako Ahaziya ali m’nyumba yake ku Samariya, anagwa+ kuchokera pachipinda chapadenga+ kudzera pachibowo chotchinga, ndipo anavulala. Atatero anatuma amithenga kuti: “Pitani kwa Baala-zebubu+ mulungu wa ku Ekironi,+ mukafunse+ ngati ndichire matenda angawa.”+

  • Amosi 1:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Ndidzapha anthu a ku Asidodi+ pamodzi ndi wogwira ndodo yachifumu wa ku Asikeloni.+ Ndidzalanga+ Ekironi+ ndipo ndidzafafaniza otsala mwa Afilisiti,”+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.’

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena