2 Kenako Ahaziya ali m’nyumba yake ku Samariya, anagwa+ kuchokera pachipinda chapadenga+ kudzera pachibowo chotchinga, ndipo anavulala. Atatero anatuma amithenga kuti: “Pitani kwa Baala-zebubu+ mulungu wa ku Ekironi,+ mukafunse+ ngati ndichire matenda angawa.”+