Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 3:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Ehudi anafika kwa mfumuyo ili yokhayokha m’chipinda chapadera chozizira bwino, chimene chinali padenga.* Pamenepo Ehudi anati: “Uthenga umene ndili nawo ndi wochokera kwa Mulungu.” Atatero, mfumuyo inanyamuka pampando wake wachifumu.

  • 1 Mafumu 17:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Koma Eliya anauza mayiyo kuti: “Bweretsa kuno mwana wakoyo.” Ndiyeno anatenga mwanayo m’manja mwa mayi ake n’kupita naye kuchipinda chapadenga.+ Chipinda chimenechi n’chimene Eliya anali kukhalamo, ndipo anagoneka mwanayo pabedi lake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena