Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 28:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Pamapeto pake, Sauli anauza atumiki ake kuti: “Ndifufuzireni mkazi waluso polankhula ndi mizimu,+ ndipo ine ndipita kukalankhula naye.” Pamenepo atumiki ake anamuuza kuti: “Ku Eni-dori alipo mkazi waluso polankhula ndi mizimu.”+

  • 1 Mafumu 14:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Utenge mitanda 10 ya mkate,+ makeke, ndi botolo+ la uchi, ndipo ukafike kwa iyeyo.+ Iye ndiye akakuuze zimene zichitikire mnyamatayu.”+

  • 2 Mafumu 8:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Mfumuyo itamva zimenezi, inauza Hazaeli kuti:+ “Tenga mphatso,+ upite kukakumana ndi munthu wa Mulungu woonayo. Ukafunsire+ mawu a Yehova kudzera mwa iye kuti, ‘Kodi ndichira matenda angawa?’”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena