Oweruza 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Nthawi ina, Samisoni anapita ku Gaza+ ndipo anaona hule kumeneko ndi kulowa m’nyumba ya huleyo.+ Oweruza 16:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Chotero Afilisiti anam’gwira ndi kum’boola maso+ n’kupita naye ku Gaza.+ Anam’manga ndi zomangira ziwiri zamkuwa,+ ndipo anakhala woyendetsa mwala wa mphero+ m’ndende.+ Amosi 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndidzatumiza moto pakhoma la Gaza+ ndipo udzanyeketsa nsanja zake zokhalamo. Machitidwe 8:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Koma mngelo wa Yehova+ analankhula kwa Filipo kuti: “Nyamuka ndi kulowera kum’mwera, kumsewu wochokera ku Yerusalemu kupita ku Gaza.” (Umenewu ndi msewu wa m’chipululu.)
21 Chotero Afilisiti anam’gwira ndi kum’boola maso+ n’kupita naye ku Gaza.+ Anam’manga ndi zomangira ziwiri zamkuwa,+ ndipo anakhala woyendetsa mwala wa mphero+ m’ndende.+
26 Koma mngelo wa Yehova+ analankhula kwa Filipo kuti: “Nyamuka ndi kulowera kum’mwera, kumsewu wochokera ku Yerusalemu kupita ku Gaza.” (Umenewu ndi msewu wa m’chipululu.)