Oweruza 16:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndiyeno olamulira ogwirizana a Afilisiti anasonkhana pamodzi kuti achite phwando lalikulu lopereka nsembe kwa Dagoni+ mulungu wawo, ndi kuchita chikondwerero, ndipo anali kunena kuti: “Mulungu wathu wapereka m’manja mwathu mdani wathu Samisoni!”+ 1 Samueli 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kumeneko anatenga likasa la Mulungu woona ndi kulilowetsa m’nyumba ya Dagoni, n’kuliika pafupi ndi fano la Dagonilo.+
23 Ndiyeno olamulira ogwirizana a Afilisiti anasonkhana pamodzi kuti achite phwando lalikulu lopereka nsembe kwa Dagoni+ mulungu wawo, ndi kuchita chikondwerero, ndipo anali kunena kuti: “Mulungu wathu wapereka m’manja mwathu mdani wathu Samisoni!”+
2 Kumeneko anatenga likasa la Mulungu woona ndi kulilowetsa m’nyumba ya Dagoni, n’kuliika pafupi ndi fano la Dagonilo.+