Oweruza 16:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndiyeno olamulira ogwirizana a Afilisiti anasonkhana pamodzi kuti achite phwando lalikulu lopereka nsembe kwa Dagoni+ mulungu wawo, ndi kuchita chikondwerero, ndipo anali kunena kuti: “Mulungu wathu wapereka m’manja mwathu mdani wathu Samisoni!”+ 1 Mbiri 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pamapeto pake, anakaika zida zakezo m’nyumba ya mulungu wawo,+ ndipo mutu wake anakaumangirira kunyumba ya Dagoni.+ Salimo 115:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mafano awo ndi opangidwa ndi siliva ndi golide,+Ntchito ya manja a munthu wochokera kufumbi.+
23 Ndiyeno olamulira ogwirizana a Afilisiti anasonkhana pamodzi kuti achite phwando lalikulu lopereka nsembe kwa Dagoni+ mulungu wawo, ndi kuchita chikondwerero, ndipo anali kunena kuti: “Mulungu wathu wapereka m’manja mwathu mdani wathu Samisoni!”+
10 Pamapeto pake, anakaika zida zakezo m’nyumba ya mulungu wawo,+ ndipo mutu wake anakaumangirira kunyumba ya Dagoni.+