8 Iwo anapitiriza kunena kuti: “Ndani mwa mafuko a Isiraeli amene sanabwere kwa Yehova ku Mizipa?”+ Pamenepo anaona kuti ku msasawo sikunabwere aliyense wochokera ku Yabesi-giliyadi+ kudzagwirizana ndi mpingowo.
12 Nthawi yomweyo, amuna olimba mtima ananyamuka ndi kuyenda usiku wonse kukachotsa mtembo wa Sauli ndi mitembo ya ana ake pakhoma la ku Beti-sani. Kenako anabwerera ku Yabesi ndi kutentha mitemboyo kumeneko.+