2 Samueli 23:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiyeno iye anati: “Sindingachite zimenezo+ inu Yehova! Kodi ndimwe magazi+ a amuna amene anaika miyoyo yawo pangozi kuti akatunge madziwa?” Choncho iye sanavomere kumwa madziwo. Izi n’zimene amuna atatu amphamvuwo anachita.
17 Ndiyeno iye anati: “Sindingachite zimenezo+ inu Yehova! Kodi ndimwe magazi+ a amuna amene anaika miyoyo yawo pangozi kuti akatunge madziwa?” Choncho iye sanavomere kumwa madziwo. Izi n’zimene amuna atatu amphamvuwo anachita.