Genesis 49:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “Kunena za Gadi, gulu la achifwamba lidzamuukira, koma iye adzawathira nkhondo, ndipo achifwambawo pothawa iye adzawakantha koopsa.+ Deuteronomo 33:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndipo kwa Gadi anati:+“Wodala ndi iye wofutukula malire a dera la Gadi.+Iye adzakhala ngati mkango,+Ndipo adzakhadzula dzanja, adzang’amba mutu paliwombo.+
19 “Kunena za Gadi, gulu la achifwamba lidzamuukira, koma iye adzawathira nkhondo, ndipo achifwambawo pothawa iye adzawakantha koopsa.+
20 Ndipo kwa Gadi anati:+“Wodala ndi iye wofutukula malire a dera la Gadi.+Iye adzakhala ngati mkango,+Ndipo adzakhadzula dzanja, adzang’amba mutu paliwombo.+