1 Mbiri 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ana a Rubeni, Agadi, ndi hafu ya fuko la Manase amene anali amuna amphamvu,+ onyamula chishango ndi lupanga, odziwa kupinda uta, ndi odziwa kumenya nkhondo, analipo asilikali 44,760.+ 1 Mbiri 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pa nkhondoyo iwo anathandizidwa moti Ahagara ndi onse amene anali nawo anaperekedwa m’manja mwawo, popeza anapempha Mulungu kuti awathandize+ ndipo iye anamva kupembedzera kwawo chifukwa anam’khulupirira.+
18 Ana a Rubeni, Agadi, ndi hafu ya fuko la Manase amene anali amuna amphamvu,+ onyamula chishango ndi lupanga, odziwa kupinda uta, ndi odziwa kumenya nkhondo, analipo asilikali 44,760.+
20 Pa nkhondoyo iwo anathandizidwa moti Ahagara ndi onse amene anali nawo anaperekedwa m’manja mwawo, popeza anapempha Mulungu kuti awathandize+ ndipo iye anamva kupembedzera kwawo chifukwa anam’khulupirira.+