Genesis 25:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma ana a adzakazi amene Abulahamu anali nawo, anawapatsa mphatso.+ Kenako, iye adakali ndi moyo, anatumiza anawo+ Kum’mawa,+ kutali ndi mwana wake Isaki.
6 Koma ana a adzakazi amene Abulahamu anali nawo, anawapatsa mphatso.+ Kenako, iye adakali ndi moyo, anatumiza anawo+ Kum’mawa,+ kutali ndi mwana wake Isaki.