1 Mbiri 15:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma Davide+ ndi akulu a Isiraeli+ ndiponso atsogoleri+a anthu 1,000 aliyense, anali kuyenda mosangalala+ kupita kunyumba kwa Obedi-edomu,+ kukatenga likasa la pangano la Yehova. Miyambo 15:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Zolingalira sizikwaniritsidwa ngati anthu sakambirana moona mtima,+ koma aphungu akachuluka zimakwaniritsidwa.+
25 Koma Davide+ ndi akulu a Isiraeli+ ndiponso atsogoleri+a anthu 1,000 aliyense, anali kuyenda mosangalala+ kupita kunyumba kwa Obedi-edomu,+ kukatenga likasa la pangano la Yehova.
22 Zolingalira sizikwaniritsidwa ngati anthu sakambirana moona mtima,+ koma aphungu akachuluka zimakwaniritsidwa.+