Yoswa 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ukachite kwa Ai ndi mfumu yake zimene unachita kwa Yeriko ndi mfumu yake.+ Koma katundu ndi ziweto za mumzindawo mukafunkhe zikakhale zanu.+ Usankhe amuna ena oti akabisale kumbuyo kwa mzindawo.”+ Salimo 18:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Iye akuphunzitsa manja anga kumenya nkhondo,+Ndipo manja anga akukunga uta wamkuwa.+
2 Ukachite kwa Ai ndi mfumu yake zimene unachita kwa Yeriko ndi mfumu yake.+ Koma katundu ndi ziweto za mumzindawo mukafunkhe zikakhale zanu.+ Usankhe amuna ena oti akabisale kumbuyo kwa mzindawo.”+