2 Mbiri 17:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Komanso analimba mtima potsatira njira+ za Yehova ndipo anachotsa m’dziko la Yuda malo okwezeka+ ndi mizati yopatulika.+
6 Komanso analimba mtima potsatira njira+ za Yehova ndipo anachotsa m’dziko la Yuda malo okwezeka+ ndi mizati yopatulika.+