1 Mafumu 22:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Yehosafati anayenda m’njira zonse za Asa bambo ake. Sanapatuke panjirazo, ndipo anapitiriza kuchita zoyenera pamaso pa Yehova.+ Koma sanachotse malo okwezeka. Anthu anali kufukizabe ndi kupereka nsembe yautsi m’malo okwezekawo.+ 2 Mbiri 20:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Koma sanachotse malo okwezeka+ ndiponso anthuwo anali asanakonze mitima yawo kuti atsatire Mulungu wa makolo awo.+
43 Yehosafati anayenda m’njira zonse za Asa bambo ake. Sanapatuke panjirazo, ndipo anapitiriza kuchita zoyenera pamaso pa Yehova.+ Koma sanachotse malo okwezeka. Anthu anali kufukizabe ndi kupereka nsembe yautsi m’malo okwezekawo.+
33 Koma sanachotse malo okwezeka+ ndiponso anthuwo anali asanakonze mitima yawo kuti atsatire Mulungu wa makolo awo.+