Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 12:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Koma muzidzapereka nsembe zanu zopsereza pamalo amene Yehova adzasankhe mu limodzi la mafuko anu, ndipo muzichita zonse zimene ndakulamulani pamalo amenewo.+

  • 1 Mafumu 14:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Ndipo nawonso anapitiriza kudzimangira malo okwezeka,+ zipilala zopatulika,+ ndi mizati yopatulika+ pamwamba pa phiri lililonse lalitali,+ ndiponso pansi pa mtengo uliwonse waukulu wa masamba obiriwira.+

  • 1 Mafumu 15:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Koma iye sanachotse+ malo okwezeka.+ Komabe, Asa anatumikira Yehova ndi mtima wathunthu masiku ake onse.+

  • 2 Mafumu 12:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Koma sanachotse malo okwezeka.+ Anthu anali kufukizabe ndi kupereka nsembe yautsi m’malo okwezekawo.

  • 2 Mafumu 14:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Koma sanachotse malo okwezeka.+ Anthu anali kufukizabe ndi kupereka nsembe yautsi m’malo okwezekawo.+

  • 2 Mafumu 15:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Koma sanachotse malo okwezeka.+ Anthu anali kufukizabe ndi kupereka nsembe yautsi m’malo okwezekawo.+

  • 2 Mafumu 18:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Ngati amuna inu mungandiuze kuti, ‘Tikudalira+ Yehova Mulungu wathu,’+ kodi si iye amene Hezekiya+ wam’chotsera malo ake okwezeka+ ndi maguwa ake ansembe, n’kuuza Yuda ndi Yerusalemu kuti, ‘Muzigwada patsogolo pa guwa lansembe ili, la ku Yerusalemu’?”’+

  • 2 Mbiri 20:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Koma sanachotse malo okwezeka+ ndiponso anthuwo anali asanakonze mitima yawo kuti atsatire Mulungu wa makolo awo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena