Numeri 33:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Mukapitikitse anthu onse a m’dzikolo, ndipo mukawononge zifaniziro zawo zonse zamiyala,+ ndi mafano awo onse achitsulo.+ Mukawonongenso malo awo onse opatulika olambirira.+ Deuteronomo 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mudzawononge+ malo onse amene ali pamapiri ataliatali, pazitunda ndi pansi pa mitengo ikuluikulu ya masamba obiriwira, pamene mitundu imene mukukailanda dziko lawo imatumikirirapo milungu yawo.+ 1 Mafumu 22:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Yehosafati anayenda m’njira zonse za Asa bambo ake. Sanapatuke panjirazo, ndipo anapitiriza kuchita zoyenera pamaso pa Yehova.+ Koma sanachotse malo okwezeka. Anthu anali kufukizabe ndi kupereka nsembe yautsi m’malo okwezekawo.+
52 Mukapitikitse anthu onse a m’dzikolo, ndipo mukawononge zifaniziro zawo zonse zamiyala,+ ndi mafano awo onse achitsulo.+ Mukawonongenso malo awo onse opatulika olambirira.+
2 Mudzawononge+ malo onse amene ali pamapiri ataliatali, pazitunda ndi pansi pa mitengo ikuluikulu ya masamba obiriwira, pamene mitundu imene mukukailanda dziko lawo imatumikirirapo milungu yawo.+
43 Yehosafati anayenda m’njira zonse za Asa bambo ake. Sanapatuke panjirazo, ndipo anapitiriza kuchita zoyenera pamaso pa Yehova.+ Koma sanachotse malo okwezeka. Anthu anali kufukizabe ndi kupereka nsembe yautsi m’malo okwezekawo.+