Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 33:52
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 52 Mukapitikitse anthu onse a m’dzikolo, ndipo mukawononge zifaniziro zawo zonse zamiyala,+ ndi mafano awo onse achitsulo.+ Mukawonongenso malo awo onse opatulika olambirira.+

  • Deuteronomo 12:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Koma muzidzapereka nsembe zanu zopsereza pamalo amene Yehova adzasankhe mu limodzi la mafuko anu, ndipo muzichita zonse zimene ndakulamulani pamalo amenewo.+

  • 2 Mbiri 6:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Koma ndidzasankha Yerusalemu+ kuti dzina langa likhale kumeneko, ndiponso ndidzasankha Davide kuti alamulire anthu anga Aisiraeli.’+

  • 2 Mbiri 32:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Kodi si Hezekiya yemweyo amene anachotsa malo ake okwezeka+ ndi maguwa ake ansembe+ kenako n’kuuza anthu a ku Yuda ndi ku Yerusalemu kuti: “Muziwerama+ pamaso pa guwa lansembe limodzi lokha+ ndipo nsembe yautsi muzifukiza pamenepo”?+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena