2 Mbiri 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kenako Yehova anaonekera+ kwa Solomo usiku n’kumuuza kuti: “Ndamva pemphero lako+ ndipo ndasankha+ malo ano kukhala nyumba yanga yoperekeramo nsembe.+
12 Kenako Yehova anaonekera+ kwa Solomo usiku n’kumuuza kuti: “Ndamva pemphero lako+ ndipo ndasankha+ malo ano kukhala nyumba yanga yoperekeramo nsembe.+