1 Mafumu 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova anaonekera kwa iye kachiwiri, mofanana ndi momwe anamuonekera ku Gibeoni.+ 2 Mbiri 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Usiku wa tsiku limenelo, Mulungu anaonekera kwa Solomo ndi kumuuza kuti: “Tandiuza, ukufuna ndikupatse chiyani?”+
7 Usiku wa tsiku limenelo, Mulungu anaonekera kwa Solomo ndi kumuuza kuti: “Tandiuza, ukufuna ndikupatse chiyani?”+