Deuteronomo 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Nsembe zanu zopsereza+ ndi nsembe zina, zopereka zanu za chakhumi,*+ chopereka chochokera m’manja mwanu,+ nsembe zanu za lonjezo,+ nsembe zanu zaufulu,+ ana oyamba kubadwa a ng’ombe ndi a nkhosa zanu,+ zonsezi muzidzazibweretsa kumalo amenewo. 2 Mbiri 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo ndani angakhale ndi mphamvu zomangira Mulunguyo nyumba?+ Pakuti kumwamba, ngakhale kumwambamwamba, ndi kosakwanira kuti akhaleko.+ Ndiye ine ndine ndani+ kuti ndimumangire nyumba, kupatulapo yofukiziramo nsembe yautsi pamaso pake?+
6 Nsembe zanu zopsereza+ ndi nsembe zina, zopereka zanu za chakhumi,*+ chopereka chochokera m’manja mwanu,+ nsembe zanu za lonjezo,+ nsembe zanu zaufulu,+ ana oyamba kubadwa a ng’ombe ndi a nkhosa zanu,+ zonsezi muzidzazibweretsa kumalo amenewo.
6 Ndipo ndani angakhale ndi mphamvu zomangira Mulunguyo nyumba?+ Pakuti kumwamba, ngakhale kumwambamwamba, ndi kosakwanira kuti akhaleko.+ Ndiye ine ndine ndani+ kuti ndimumangire nyumba, kupatulapo yofukiziramo nsembe yautsi pamaso pake?+