2 Samueli 7:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamenepo Mfumu Davide inabwera ndi kukhala pansi pamaso pa Yehova, ndipo inati: “Ndine yani ine,+ Yehova Ambuye Wamkulu Koposa? Ndipo nyumba yanga n’chiyani kuti mundifikitse pamene ndili pano? 1 Mbiri 29:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Ndine ndani ine,+ ndipo anthu anga ndani kuti tithe kupereka nsembe zaufulu ngati zimenezi?+ Pakuti chilichonse n’chochokera kwa inu,+ ndipo tapereka kwa inu zochokera m’dzanja lanu.
18 Pamenepo Mfumu Davide inabwera ndi kukhala pansi pamaso pa Yehova, ndipo inati: “Ndine yani ine,+ Yehova Ambuye Wamkulu Koposa? Ndipo nyumba yanga n’chiyani kuti mundifikitse pamene ndili pano?
14 “Ndine ndani ine,+ ndipo anthu anga ndani kuti tithe kupereka nsembe zaufulu ngati zimenezi?+ Pakuti chilichonse n’chochokera kwa inu,+ ndipo tapereka kwa inu zochokera m’dzanja lanu.