Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 32:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ine ndine wosayenerera kukoma mtima kosatha ndi kukhulupirika konseku, kumene mwandionetsa ine mtumiki wanu.+ Ndinawoloka Yorodano ndilibe kanthu, koma ndodo yokha, ndipo tsopano ndili ndi magulu awiriwa.+

  • 1 Samueli 2:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Iye amadzutsa wonyozeka, kumuchotsa pafumbi.+

      Amachotsa osauka padzala,+

      Kuti awakhazike pakati pa anthu olemekezeka,+ ndipo amawapatsa mpando wachifumu waulemerero.+

      Pakuti michirikizo ya dziko lapansi ndi ya Yehova,+

      Ndipo anakhazika dziko lapansi pamichirikizo imeneyo.

  • 1 Samueli 18:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Koma Davide anayankha Sauli kuti: “Ndine yani ine, ndipo abale anga, anthu a m’banja la bambo anga ndani mu Isiraeli monse muno kuti ndikhale mkamwini wa mfumu?”+

  • 1 Mbiri 17:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Pamenepo Mfumu Davide inabwera ndi kukhala pansi pamaso pa Yehova,+ ndipo inati: “Ndine yani ine,+ inu Yehova Mulungu? Ndipo nyumba yanga n’chiyani+ kuti mundifikitse pamene ndili pano?+

  • Mika 6:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Iwe munthu wochokera kufumbi, iye anakuuza zimene zili zabwino.+ Kodi Yehova akufuna chiyani kwa iwe? Iye akufuna kuti uzichita chilungamo,+ ukhale wokoma mtima+ ndiponso uziyenda modzichepetsa+ ndi Mulungu wako.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena