Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 20:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 “Bwerera, kauze Hezekiya mtsogoleri+ wa anthu anga kuti, ‘Yehova Mulungu+ wa Davide kholo lako wanena kuti: “Ndamva+ pemphero lako,+ ndipo ndaona misozi yako.+ Ndikuchiritsa.+ Pa tsiku lachitatu udzapita kunyumba ya Yehova.+

  • Salimo 66:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Ndithudi, Mulungu wamva,+

      Wamvetsera mwatcheru mawu a pemphero langa.+

  • Luka 1:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Koma mngeloyo anamuuza kuti: “Usachite mantha Zekariya, chifukwa pembedzero lako lamveka ndithu.+ Mkazi wako Elizabeti adzakuberekera mwana wamwamuna, ndipo udzamutche Yohane.+

  • Machitidwe 10:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Munthuyo anandiuza kuti, ‘Koneliyo, Mulungu wamva pemphero lako, ndipo wakumbukira mphatso zako zachifundo.+

  • 1 Petulo 3:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Pakuti maso+ a Yehova* ali pa olungama, ndipo makutu ake amamva pembedzero lawo,+ koma nkhope ya Yehova imakwiyira anthu ochita zoipa.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena