1 Samueli 14:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Zitatero, Sauli anamangira Yehova guwa lansembe,+ limene linali guwa lake loyamba kumangira Yehova.+ 1 Mafumu 22:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Yehosafati anayenda m’njira zonse za Asa bambo ake. Sanapatuke panjirazo, ndipo anapitiriza kuchita zoyenera pamaso pa Yehova.+ Koma sanachotse malo okwezeka. Anthu anali kufukizabe ndi kupereka nsembe yautsi m’malo okwezekawo.+ 2 Mafumu 14:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma sanachotse malo okwezeka.+ Anthu anali kufukizabe ndi kupereka nsembe yautsi m’malo okwezekawo.+
35 Zitatero, Sauli anamangira Yehova guwa lansembe,+ limene linali guwa lake loyamba kumangira Yehova.+
43 Yehosafati anayenda m’njira zonse za Asa bambo ake. Sanapatuke panjirazo, ndipo anapitiriza kuchita zoyenera pamaso pa Yehova.+ Koma sanachotse malo okwezeka. Anthu anali kufukizabe ndi kupereka nsembe yautsi m’malo okwezekawo.+
4 Koma sanachotse malo okwezeka.+ Anthu anali kufukizabe ndi kupereka nsembe yautsi m’malo okwezekawo.+