1 Samueli 7:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Akazungulirazungulira, anali kubwerera ku Rama,+ chifukwa kumeneko n’kumene kunali nyumba yake, ndipo anali kuweruza Isiraeli ali kumeneko. Komanso iye anamangira Yehova guwa lansembe kumeneko.+ 2 Samueli 24:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako Gadi anafika kwa Davide tsiku limenelo ndi kumuuza kuti: “Pita ukamangire Yehova guwa lansembe pamalo opunthira mbewu a Arauna Myebusi.”+ 2 Samueli 24:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Zitatero, Davide anamangira Yehova guwa lansembe+ pamenepo ndipo anapereka nsembe zopsereza ndi nsembe zachiyanjano. Choncho Yehova anamva kuchonderera kwawo,+ moti mliriwo anauthetsa mu Isiraeli.
17 Akazungulirazungulira, anali kubwerera ku Rama,+ chifukwa kumeneko n’kumene kunali nyumba yake, ndipo anali kuweruza Isiraeli ali kumeneko. Komanso iye anamangira Yehova guwa lansembe kumeneko.+
18 Kenako Gadi anafika kwa Davide tsiku limenelo ndi kumuuza kuti: “Pita ukamangire Yehova guwa lansembe pamalo opunthira mbewu a Arauna Myebusi.”+
25 Zitatero, Davide anamangira Yehova guwa lansembe+ pamenepo ndipo anapereka nsembe zopsereza ndi nsembe zachiyanjano. Choncho Yehova anamva kuchonderera kwawo,+ moti mliriwo anauthetsa mu Isiraeli.