Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 15:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Koma iye sanachotse+ malo okwezeka.+ Komabe, Asa anatumikira Yehova ndi mtima wathunthu masiku ake onse.+

  • 1 Mafumu 22:43
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 43 Yehosafati anayenda m’njira zonse za Asa bambo ake. Sanapatuke panjirazo, ndipo anapitiriza kuchita zoyenera pamaso pa Yehova.+ Koma sanachotse malo okwezeka. Anthu anali kufukizabe ndi kupereka nsembe yautsi m’malo okwezekawo.+

  • 2 Mbiri 17:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Komanso analimba mtima potsatira njira+ za Yehova ndipo anachotsa m’dziko la Yuda malo okwezeka+ ndi mizati yopatulika.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena