Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 18:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Pakuti ndasunga njira za Yehova,+

      Sindinachoke kwa Mulungu wanga. Ndikanatero, ndikanachita chinthu choipa.+

  • Salimo 119:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 119 Odala ndi anthu osalakwitsa kanthu m’njira zawo,+

      Anthu amene akutsatira chilamulo cha Yehova.+

  • Hoseya 14:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ndani ali ndi nzeru kuti amvetse zinthu zimenezi?+ Wochenjera ndani kuti adziwe zimenezi?+ Pakuti njira za Yehova ndi zowongoka+ ndipo anthu olungama ndi amene adzayendamo,+ koma olakwa adzapunthwa m’njira zimenezo.+

  • Yohane 2:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Choncho anapanga mkwapulo wazingwe, n’kuthamangitsa onse amene anali ndi nkhosa ndi ng’ombe ndipo anawatulutsa m’kachisimo. Anakhuthula makobidi a osintha ndalama ndi kugubuduza matebulo awo.+

  • Machitidwe 4:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Atatha kupembedzera, malo amene anasonkhanawo anagwedezeka.+ Pamenepo aliyense wa iwo anadzazidwa ndi mzimu woyera,+ ndipo anayamba kulankhula mawu a Mulungu molimba mtima.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena