1 Samueli 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iwo anawayankha kuti: “Ee, alipo. Mum’peza kumene mukupitaku. Fulumirani, wafika lero mumzinda chifukwa lero anthu apereka nsembe+ pamalo okwezeka.+
12 Iwo anawayankha kuti: “Ee, alipo. Mum’peza kumene mukupitaku. Fulumirani, wafika lero mumzinda chifukwa lero anthu apereka nsembe+ pamalo okwezeka.+