Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 31:54
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 54 Pambuyo pake, Yakobo anapereka nsembe m’phirimo n’kuitana abale ake kuti adye chakudya.+ Motero iwo anadya chakudya n’kugona m’phirimo usiku umenewo.

  • 1 Samueli 7:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ndiyeno Samueli anatenga mwana wa nkhosa woyamwa ndi kum’pereka nsembe yopsereza, nsembe yathunthu,+ kwa Yehova. Atatero anayamba kupempherera Aisiraeli+ kwa Yehova kuti awathandize, ndipo Yehova anamuyankha.+

  • 1 Samueli 16:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Iye anayankha kuti: “Inde, n’kwabwino. Ndabwera kudzapereka nsembe kwa Yehova. Dziyeretseni,+ ndipo mupite nane kopereka nsembe.” Chotero iye anayeretsa Jese ndi ana ake, kenako anawaitanira kopereka nsembe.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena