1 Mafumu 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Anthuwo anali kupereka nsembe pamalo okwezeka,+ chifukwa anali asanamange nyumba ya dzina la Yehova mpaka masiku amenewo.+ 1 Mbiri 16:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Anasiyanso Zadoki+ wansembe ndi abale ake ansembe kuchihema cha Yehova chimene chinali pamalo okwezeka a ku Gibeoni,+ 2 Mbiri 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako Solomo ndi mpingo wonsewo anapitira limodzi kumalo okwezeka a ku Gibeoni.+ Anapita kumeneko chifukwa ndi kumene kunali chihema chokumanako+ cha Mulungu woona, chimene Mose mtumiki+ wa Yehova anapanga m’chipululu.
2 Anthuwo anali kupereka nsembe pamalo okwezeka,+ chifukwa anali asanamange nyumba ya dzina la Yehova mpaka masiku amenewo.+
39 Anasiyanso Zadoki+ wansembe ndi abale ake ansembe kuchihema cha Yehova chimene chinali pamalo okwezeka a ku Gibeoni,+
3 Kenako Solomo ndi mpingo wonsewo anapitira limodzi kumalo okwezeka a ku Gibeoni.+ Anapita kumeneko chifukwa ndi kumene kunali chihema chokumanako+ cha Mulungu woona, chimene Mose mtumiki+ wa Yehova anapanga m’chipululu.