1 Mafumu 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Inuyo mukudziwa bwino kuti Davide bambo anga sanathe kumanga nyumba ya dzina la Yehova Mulungu wake, chifukwa cha nkhondo+ zimene adani ake ankamenyana naye m’madera onse omuzungulira, mpaka pamene Yehova anaika adani akewo pansi pa mapazi ake. 1 Mbiri 17:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Pita, ukauze Davide mtumiki wanga kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Si iwe amene udzandimangira nyumba yokhalamo.+ 1 Mbiri 17:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iye ndiye adzandimangire nyumba,+ ndipo ndithu ndidzakhazikitsa mpando wake wachifumu mpaka kalekale.+ 1 Mbiri 28:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Kuwonjezera pamenepo, anandiuza kuti: ‘Mwana wako Solomo ndiye adzamanga nyumba yanga+ ndiponso mabwalo anga, chifukwa ndam’sankha kuti akhale mwana wanga+ ndipo ine ndidzakhala atate wake.+ Machitidwe 7:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Koma Solomo ndiye anamangira Mulungu nyumba.+
3 “Inuyo mukudziwa bwino kuti Davide bambo anga sanathe kumanga nyumba ya dzina la Yehova Mulungu wake, chifukwa cha nkhondo+ zimene adani ake ankamenyana naye m’madera onse omuzungulira, mpaka pamene Yehova anaika adani akewo pansi pa mapazi ake.
4 “Pita, ukauze Davide mtumiki wanga kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Si iwe amene udzandimangira nyumba yokhalamo.+
12 Iye ndiye adzandimangire nyumba,+ ndipo ndithu ndidzakhazikitsa mpando wake wachifumu mpaka kalekale.+
6 “Kuwonjezera pamenepo, anandiuza kuti: ‘Mwana wako Solomo ndiye adzamanga nyumba yanga+ ndiponso mabwalo anga, chifukwa ndam’sankha kuti akhale mwana wanga+ ndipo ine ndidzakhala atate wake.+