1 Mafumu 6:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Nyumba yonseyo anaikuta ndi golide+ mpaka kuimaliza, ndipo guwa lansembe lonse,+ lomwe linali kufupi ndi chipinda chamkati, analikuta ndi golide.+ 1 Mbiri 29:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chumacho chili motere: Matalente* 3,000 a golide wa ku Ofiri,+ matalente 7,000 a siliva woyengedwa bwino wokutira makoma a nyumbazo,
22 Nyumba yonseyo anaikuta ndi golide+ mpaka kuimaliza, ndipo guwa lansembe lonse,+ lomwe linali kufupi ndi chipinda chamkati, analikuta ndi golide.+
4 Chumacho chili motere: Matalente* 3,000 a golide wa ku Ofiri,+ matalente 7,000 a siliva woyengedwa bwino wokutira makoma a nyumbazo,