1 Mbiri 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano Davide anakambirana ndi mkulu aliyense wa anthu 1,000, wa anthu 100 ndiponso mtsogoleri aliyense.+ Miyambo 11:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pakakhala popanda malangizo anzeru, anthu amagwa.+ Koma pakakhala aphungu ochuluka anthu amapulumuka.+
13 Tsopano Davide anakambirana ndi mkulu aliyense wa anthu 1,000, wa anthu 100 ndiponso mtsogoleri aliyense.+
14 Pakakhala popanda malangizo anzeru, anthu amagwa.+ Koma pakakhala aphungu ochuluka anthu amapulumuka.+