1 Mbiri 16:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 M’patseni Yehova ulemerero wa dzina lake,+Tengani mphatso n’kubwera nayo pamaso pake.+Gwadirani Yehova mutavala zovala zokongola ndi zopatulika.+ Salimo 29:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 M’patseni Yehova ulemerero woyenera dzina lake.+Weramirani Yehova mutavala zovala zopatulika zokongola.+ Salimo 96:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Gwadirani Yehova mutavala zovala zokongola ndi zopatulika.+Njenjemerani ndi mantha aakulu* pamaso pake, inu anthu nonse okhala padziko lapansi.+
29 M’patseni Yehova ulemerero wa dzina lake,+Tengani mphatso n’kubwera nayo pamaso pake.+Gwadirani Yehova mutavala zovala zokongola ndi zopatulika.+
2 M’patseni Yehova ulemerero woyenera dzina lake.+Weramirani Yehova mutavala zovala zopatulika zokongola.+
9 Gwadirani Yehova mutavala zovala zokongola ndi zopatulika.+Njenjemerani ndi mantha aakulu* pamaso pake, inu anthu nonse okhala padziko lapansi.+