1 Mafumu 16:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Omuri anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova, ndipo anachita zoipa kwambiri kuposa onse amene anakhalapo iye asanakhale.+ 1 Mafumu 16:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ahabu anaimikanso mzati wopatulika,+ ndipo iye anachita zinthu zambiri zokwiyitsa+ Yehova Mulungu wa Isiraeli kuposa mafumu onse a Isiraeli amene anakhalapo iye asanakhale.
25 Omuri anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova, ndipo anachita zoipa kwambiri kuposa onse amene anakhalapo iye asanakhale.+
33 Ahabu anaimikanso mzati wopatulika,+ ndipo iye anachita zinthu zambiri zokwiyitsa+ Yehova Mulungu wa Isiraeli kuposa mafumu onse a Isiraeli amene anakhalapo iye asanakhale.