1 Mafumu 16:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pomalizira pake Omuri anagona pamodzi ndi makolo ake ndipo anamuika m’manda ku Samariya. Kenako Ahabu+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.
28 Pomalizira pake Omuri anagona pamodzi ndi makolo ake ndipo anamuika m’manda ku Samariya. Kenako Ahabu+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.