1 Mafumu 1:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Atatero anthuwo anayamba kumulondola ndipo anali kuimba zitoliro+ ndi kusangalala kwambiri,+ moti nthaka+ inang’ambika chifukwa cha phokoso lawo. Miyambo 11:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mudzi umakondwera chifukwa cha makhalidwe abwino a anthu olungama,+ koma anthu oipa akawonongeka pamakhala mfuu yachisangalalo.+
40 Atatero anthuwo anayamba kumulondola ndipo anali kuimba zitoliro+ ndi kusangalala kwambiri,+ moti nthaka+ inang’ambika chifukwa cha phokoso lawo.
10 Mudzi umakondwera chifukwa cha makhalidwe abwino a anthu olungama,+ koma anthu oipa akawonongeka pamakhala mfuu yachisangalalo.+