1 Mafumu 1:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Tsopano wansembe Zadoki anatenga nyanga ya mafuta+ m’chihema+ n’kudzoza+ Solomo. Ndiyeno anthuwo anayamba kuliza lipenga ndipo anthu onse anafuula kuti: “Mfumu Solomo ikhale ndi moyo wautali!”+ 2 Mafumu 9:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anthuwo atamva zimenezi, msangamsanga aliyense anavula malaya ake+ n’kumuyalira pamasitepe popanda kanthu. Kenako anayamba kuliza malipenga,+ ndipo anali kunena kuti: “Yehu wakhala mfumu!”+
39 Tsopano wansembe Zadoki anatenga nyanga ya mafuta+ m’chihema+ n’kudzoza+ Solomo. Ndiyeno anthuwo anayamba kuliza lipenga ndipo anthu onse anafuula kuti: “Mfumu Solomo ikhale ndi moyo wautali!”+
13 Anthuwo atamva zimenezi, msangamsanga aliyense anavula malaya ake+ n’kumuyalira pamasitepe popanda kanthu. Kenako anayamba kuliza malipenga,+ ndipo anali kunena kuti: “Yehu wakhala mfumu!”+