2 Mbiri 22:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ahaziya nayenso anayenda m’njira za anthu a m’nyumba ya Ahabu+ chifukwa amayi ake+ ndi amene anali kumulangiza kuti azichita zoipa.
3 Ahaziya nayenso anayenda m’njira za anthu a m’nyumba ya Ahabu+ chifukwa amayi ake+ ndi amene anali kumulangiza kuti azichita zoipa.