Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 16:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Ahabu anaimikanso mzati wopatulika,+ ndipo iye anachita zinthu zambiri zokwiyitsa+ Yehova Mulungu wa Isiraeli kuposa mafumu onse a Isiraeli amene anakhalapo iye asanakhale.

  • 2 Mafumu 8:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Iye anayenda m’njira ya anthu a m’nyumba ya Ahabu,+ ndipo anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova+ monga mmene anachitira a m’nyumba ya Ahabu, chifukwa anali wachibale wa nyumba ya Ahabu.+

  • Mika 6:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Anthu inu mukutsatira zochita za Omuri.+ Zochita zonse za anthu a nyumba ya Ahabu, inunso mukuzichita+ ndipo mukuyendera maganizo awo.+ Pa chifukwa chimenechi ndidzakusandutsani chinthu chodabwitsa ndipo anthu a mumzindawo adzakhala oyenera kuwaimbira mluzu.+ Inuyo mudzatonzedwa ndi mitundu ina ya anthu.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena