1 Mafumu 16:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ahabu anaimikanso mzati wopatulika,+ ndipo iye anachita zinthu zambiri zokwiyitsa+ Yehova Mulungu wa Isiraeli kuposa mafumu onse a Isiraeli amene anakhalapo iye asanakhale. 2 Mbiri 22:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ahaziya nayenso anayenda m’njira za anthu a m’nyumba ya Ahabu+ chifukwa amayi ake+ ndi amene anali kumulangiza kuti azichita zoipa.
33 Ahabu anaimikanso mzati wopatulika,+ ndipo iye anachita zinthu zambiri zokwiyitsa+ Yehova Mulungu wa Isiraeli kuposa mafumu onse a Isiraeli amene anakhalapo iye asanakhale.
3 Ahaziya nayenso anayenda m’njira za anthu a m’nyumba ya Ahabu+ chifukwa amayi ake+ ndi amene anali kumulangiza kuti azichita zoipa.