2 Mbiri 22:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anapitiriza kubisidwa m’nyumba ya Mulungu woona zaka 6,+ pamene Ataliya+ anali mfumukazi ya dzikolo.+ 2 Mbiri 24:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pajatu ana+ a Ataliya mkazi woipa uja anathyola nyumba ya Mulungu woona,+ n’kutenga zinthu zonse zopatulika+ za m’nyumba ya Yehovayo n’kukazipereka kwa Abaala.”+
12 Anapitiriza kubisidwa m’nyumba ya Mulungu woona zaka 6,+ pamene Ataliya+ anali mfumukazi ya dzikolo.+
7 Pajatu ana+ a Ataliya mkazi woipa uja anathyola nyumba ya Mulungu woona,+ n’kutenga zinthu zonse zopatulika+ za m’nyumba ya Yehovayo n’kukazipereka kwa Abaala.”+