Deuteronomo 32:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Iwo anali kupereka nsembe kwa ziwanda, osati kwa Mulungu.+Anapereka nsembe kwa milungu imene sanaidziwe,+Milungu yatsopano yongobwera kumene,+Imene makolo anu akale sanaidziwe. Ezekieli 16:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Unali kutenga zinthu zako zokongola zochokera pagolide ndi siliva wanga amene ndinakupatsa+ n’kupangira zifaniziro za munthu wamwamuna+ n’kumachita nazo uhule.+ Hoseya 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndiyeno ndidzamuimba mlandu+ chifukwa cha masiku amene anapembedza zifaniziro za Baala+ zimene anali kuzifukizira nsembe zautsi.+ Nthawi imeneyi anali kuvala mphete* yake ndi zinthu zake zodzikongoletsera.+ Iye anali kutsatira amuna omukonda kwambiri+ ndipo ine anandiiwala,’+ watero Yehova.
17 Iwo anali kupereka nsembe kwa ziwanda, osati kwa Mulungu.+Anapereka nsembe kwa milungu imene sanaidziwe,+Milungu yatsopano yongobwera kumene,+Imene makolo anu akale sanaidziwe.
17 Unali kutenga zinthu zako zokongola zochokera pagolide ndi siliva wanga amene ndinakupatsa+ n’kupangira zifaniziro za munthu wamwamuna+ n’kumachita nazo uhule.+
13 Ndiyeno ndidzamuimba mlandu+ chifukwa cha masiku amene anapembedza zifaniziro za Baala+ zimene anali kuzifukizira nsembe zautsi.+ Nthawi imeneyi anali kuvala mphete* yake ndi zinthu zake zodzikongoletsera.+ Iye anali kutsatira amuna omukonda kwambiri+ ndipo ine anandiiwala,’+ watero Yehova.