Yesaya 17:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Popeza waiwala+ Mulungu wa chipulumutso chako,+ ndipo Thanthwe+ la chitetezo chako sunalikumbukire, n’chifukwa chake ukulima minda yokongola n’kumabzalamo mphukira ya mlendo. Yeremiya 2:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Kodi namwali angaiwale zodzikongoletsera? Kodi mkwatibwi angaiwale lamba wake wa pachifuwa? Koma anthu anga andiiwala kwa masiku osawerengeka.+ Ezekieli 22:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anthu alandira ziphuphu kuti akhetse magazi.+ Iwe walandira chiwongoladzanja+ ndi kuchita katapira.+ Ukupeza phindu losayenera mwa kubera anzako+ mwachinyengo+ ndipo ine wandiiwala,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.
10 Popeza waiwala+ Mulungu wa chipulumutso chako,+ ndipo Thanthwe+ la chitetezo chako sunalikumbukire, n’chifukwa chake ukulima minda yokongola n’kumabzalamo mphukira ya mlendo.
32 Kodi namwali angaiwale zodzikongoletsera? Kodi mkwatibwi angaiwale lamba wake wa pachifuwa? Koma anthu anga andiiwala kwa masiku osawerengeka.+
12 Anthu alandira ziphuphu kuti akhetse magazi.+ Iwe walandira chiwongoladzanja+ ndi kuchita katapira.+ Ukupeza phindu losayenera mwa kubera anzako+ mwachinyengo+ ndipo ine wandiiwala,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.