Ekisodo 32:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamenepo Aroni anawauza kuti: “Vulani ndolo* zagolide+ zimene avala akazi anu, ana anu aamuna ndi ana anu aakazi, ndipo mubwere nazo kwa ine.” Yeremiya 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Akatero amakongoletsa fanolo ndi siliva komanso golide.+ Kenako amatenga nyundo ndi kukhomerera mafanowo pansi ndi misomali kuti asagwe.+
2 Pamenepo Aroni anawauza kuti: “Vulani ndolo* zagolide+ zimene avala akazi anu, ana anu aamuna ndi ana anu aakazi, ndipo mubwere nazo kwa ine.”
4 Akatero amakongoletsa fanolo ndi siliva komanso golide.+ Kenako amatenga nyundo ndi kukhomerera mafanowo pansi ndi misomali kuti asagwe.+