Yeremiya 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kodi mungamabe,+ kupha,+ kuchita chigololo,+ kulumbira monama,+ kufukiza nsembe zautsi kwa Baala+ ndi kutsatira milungu ina imene simunali kuidziwa,+ Yeremiya 18:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pakuti anthu anga andiiwala+ moti amapereka nsembe zautsi kwa chinthu chopanda pake,+ ndiponso amapunthwitsa anthu amene akuyenda panjira zawo,+ m’njira zakale,+ ndi kuwayendetsa m’njira zina, njira zokumbikakumbika. Hoseya 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Pamene iye anali kuitanidwa kwambiri,+ m’pamenenso anapitiriza kuchoka.+ Anayamba kupereka nsembe kwa zifaniziro za Baala+ ndipo anayamba kufukiza nsembe zautsi kwa zifaniziro zogoba.+
9 Kodi mungamabe,+ kupha,+ kuchita chigololo,+ kulumbira monama,+ kufukiza nsembe zautsi kwa Baala+ ndi kutsatira milungu ina imene simunali kuidziwa,+
15 Pakuti anthu anga andiiwala+ moti amapereka nsembe zautsi kwa chinthu chopanda pake,+ ndiponso amapunthwitsa anthu amene akuyenda panjira zawo,+ m’njira zakale,+ ndi kuwayendetsa m’njira zina, njira zokumbikakumbika.
2 “Pamene iye anali kuitanidwa kwambiri,+ m’pamenenso anapitiriza kuchoka.+ Anayamba kupereka nsembe kwa zifaniziro za Baala+ ndipo anayamba kufukiza nsembe zautsi kwa zifaniziro zogoba.+