Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 57:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Unaika chizindikiro chachikumbutso chako kuseri kwa chitseko ndi kuseri kwa felemu.+ Iwe unavula n’kukwera mtunda kupita kumeneko uli kutali ndi ine. Unakulitsa bedi lako,+ ndipo unachita nawo pangano. Unkakonda kugona nawo pabedi+ ndipo unaona chiwalo cha mwamuna.

  • Ezekieli 16:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Unayamba kuchita uhule ndi ana aamuna a Iguputo,+ anthu a ziwalo zikuluzikulu amene ukukhala nawo pafupi.+ Unapitiriza kuwonjezera uhule wako kuti undikwiyitse.

  • Ezekieli 23:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Iye anali ndi chilakolako champhamvu ngati cha adzakazi* amene amuna awo ali ndi ziwalo ngati za abulu amphongo, amuna amene mpheto zawo zili ngati mpheto za mahatchi amphongo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena