Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 23:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Yehova Mulungu wa Isiraeli wadzudzula abusa amene akuweta anthu ake kuti: “Inu mwabalalitsa nkhosa zanga. Mukupitiriza kuzimwaza ndipo simukuzisamalira.”+

      “Tsopano ndikutembenukira kwa inu chifukwa cha zochita zanu zoipazo,”+ watero Yehova.

  • Amosi 3:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 ‘Pa mabanja onse apadziko lapansi+ ine ndimadziwa inu nokha.+ Choncho ndidzakulangani chifukwa cha zolakwa zanu zonse.+

  • Zekariya 10:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 “Mkwiyo wanga wayakira abusa,+ ndipo atsogoleri awo oipa ngati mbuzi+ ndiwaimba mlandu.+ Pakuti ine Yehova wa makamu ndacheukira gulu langa la nkhosa.+ Ndacheukira nyumba ya Yuda ndipo ndaisandutsa hatchi+ yanga yaulemerero, yokwera popita kunkhondo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena